Yoswa 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Yehova anauza Yoswa kuti: “Lero ndachotsa chitonzo cha Iguputo pa inu.”+ Chotero malowo anayamba kuwatchula kuti Giligala,+ kufikira lero. Yoswa 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anakafika ku Debiri kuchigwa cha Akori+ n’kukhotera kumpoto cha ku Giligala,+ patsogolo pa chitunda cha Adumi, kum’mwera kwa chigwa cha mtsinje. Malirewo anapitirira n’kukafika kumadzi a Eni-semesi,+ n’kukathera ku Eni-rogeli.+
9 Kenako Yehova anauza Yoswa kuti: “Lero ndachotsa chitonzo cha Iguputo pa inu.”+ Chotero malowo anayamba kuwatchula kuti Giligala,+ kufikira lero.
7 Anakafika ku Debiri kuchigwa cha Akori+ n’kukhotera kumpoto cha ku Giligala,+ patsogolo pa chitunda cha Adumi, kum’mwera kwa chigwa cha mtsinje. Malirewo anapitirira n’kukafika kumadzi a Eni-semesi,+ n’kukathera ku Eni-rogeli.+