Yoswa 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Anthuwo anawoloka mtsinje wa Yorodano pa tsiku la 10 la mwezi woyamba, ndipo anakamanga msasa ku Giligala,+ kumalire a kum’mawa kwa Yeriko. Yoswa 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero Yoswa anapanga timipeni tamiyala, ndipo anadula khungu la ana a Isiraeli. Zimenezi zinachitikira ku Gibeyati-haaraloti.+
19 Anthuwo anawoloka mtsinje wa Yorodano pa tsiku la 10 la mwezi woyamba, ndipo anakamanga msasa ku Giligala,+ kumalire a kum’mawa kwa Yeriko.
3 Chotero Yoswa anapanga timipeni tamiyala, ndipo anadula khungu la ana a Isiraeli. Zimenezi zinachitikira ku Gibeyati-haaraloti.+