Yoswa 21:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kuchokera m’fuko la Benjamini, anawapatsa Gibeoni+ ndi malo ake odyetserako ziweto, Geba+ ndi malo ake odyetserako ziweto, 1 Mbiri 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Panalinso ana a Ehudi amene anali atsogoleri a nyumba za makolo a anthu okhala ku Geba.+ Iwowa anagwira anthu ndi kuwatengera ku Manahati. Nehemiya 11:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ana a Benjamini anakhala ku Geba,+ Mikimasi,+ Aiya,+ Beteli+ ndi midzi yake yozungulira,
17 Kuchokera m’fuko la Benjamini, anawapatsa Gibeoni+ ndi malo ake odyetserako ziweto, Geba+ ndi malo ake odyetserako ziweto,
6 Panalinso ana a Ehudi amene anali atsogoleri a nyumba za makolo a anthu okhala ku Geba.+ Iwowa anagwira anthu ndi kuwatengera ku Manahati.