Genesis 28:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako, malowo anawatcha Beteli.+ Koma dzina lakale la mzindawo linali Luzi.+ Yoswa 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Malirewo anapitirira kukafika ku Luzi,+ kutanthauza Beteli.+ Anakafika kum’mwera kwa malo otsetsereka otchedwa Luzi, n’kutsetserekera ku Ataroti-adara,+ n’kukadutsa paphiri la kum’mwera kwa Beti-horoni Wakumunsi.+
13 Malirewo anapitirira kukafika ku Luzi,+ kutanthauza Beteli.+ Anakafika kum’mwera kwa malo otsetsereka otchedwa Luzi, n’kutsetserekera ku Ataroti-adara,+ n’kukadutsa paphiri la kum’mwera kwa Beti-horoni Wakumunsi.+