Genesis 35:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Potsirizira pake Yakobo anafika ku Luzi+ komwe ndi ku Beteli, m’dziko la Kanani. Iye anafika kumeneko pamodzi ndi anthu onse amene anali naye. Yoswa 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Atachoka ku Beteli wa ku Luzi,+ malirewo anakadutsa kumalire a Aareki+ ku Ataroti. Oweruza 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamenepo a nyumba ya Yosefe anayamba kuchita ukazitape+ pamzinda wa Beteli (poyamba dzina la mzindawu linali Luzi).+
6 Potsirizira pake Yakobo anafika ku Luzi+ komwe ndi ku Beteli, m’dziko la Kanani. Iye anafika kumeneko pamodzi ndi anthu onse amene anali naye.
23 Pamenepo a nyumba ya Yosefe anayamba kuchita ukazitape+ pamzinda wa Beteli (poyamba dzina la mzindawu linali Luzi).+