1 Mbiri 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atatero, Alevi anawerengedwa kuyambira azaka 30 kupita m’tsogolo.+ Anawerenga mwamuna aliyense wamphamvu, mmodzi ndi mmodzi,* ndipo onse anakwana 38,000.
3 Atatero, Alevi anawerengedwa kuyambira azaka 30 kupita m’tsogolo.+ Anawerenga mwamuna aliyense wamphamvu, mmodzi ndi mmodzi,* ndipo onse anakwana 38,000.