1 Mbiri 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano anagawa ana a Aroni m’magulu awo. Ana a Aroni anali Nadabu,+ Abihu,+ Eleazara,+ ndi Itamara.+ 2 Mbiri 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano ansembe anatuluka m’malo oyera (chifukwa ansembe onse amene analipo anali atadziyeretsa+ ndipo panalibe chifukwa choti atumikire motsatira magulu awo).+ Luka 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 M’masiku a Herode,*+ mfumu ya Yudeya, kunali wansembe wina wotchedwa Zekariya wa m’gulu la ansembe lotchedwa Abiya.+ Iyeyu anali ndi mkazi wochokera mwa ana aakazi a Aroni,+ dzina lake Elizabeti.
24 Tsopano anagawa ana a Aroni m’magulu awo. Ana a Aroni anali Nadabu,+ Abihu,+ Eleazara,+ ndi Itamara.+
11 Tsopano ansembe anatuluka m’malo oyera (chifukwa ansembe onse amene analipo anali atadziyeretsa+ ndipo panalibe chifukwa choti atumikire motsatira magulu awo).+
5 M’masiku a Herode,*+ mfumu ya Yudeya, kunali wansembe wina wotchedwa Zekariya wa m’gulu la ansembe lotchedwa Abiya.+ Iyeyu anali ndi mkazi wochokera mwa ana aakazi a Aroni,+ dzina lake Elizabeti.