1 Mbiri 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano anagawa ana a Aroni m’magulu awo. Ana a Aroni anali Nadabu,+ Abihu,+ Eleazara,+ ndi Itamara.+ 2 Mbiri 35:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Konzekerani potsatira nyumba ya makolo anu+ mogwirizana ndi magulu anu,+ malinga ndi zimene analemba+ Davide mfumu ya Isiraeli ndiponso zimene analemba+ Solomo mwana wake.
24 Tsopano anagawa ana a Aroni m’magulu awo. Ana a Aroni anali Nadabu,+ Abihu,+ Eleazara,+ ndi Itamara.+
4 Konzekerani potsatira nyumba ya makolo anu+ mogwirizana ndi magulu anu,+ malinga ndi zimene analemba+ Davide mfumu ya Isiraeli ndiponso zimene analemba+ Solomo mwana wake.