Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 19:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndipo Yehova anauza Mose kuti: “Pita kwa anthu, uwayeretse lero ndi mawa, ndipo achape zovala zawo.+

  • Numeri 8:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Aleviwo anadziyeretsa+ n’kuchapa zovala zawo. Pambuyo pake, Aroni anawauza kuti ayende uku ndi uku monga nsembe yoweyula pamaso pa Yehova.+ Kenako Aroniyo anawaphimbira machimo awo kuti awayeretse.+

  • 2 Mbiri 29:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Koma ansembe+ anali ochepa kwambiri ndipo sanathe kusenda nyama zonse za nsembe zopsereza.+ Choncho abale awo+ Alevi anawathandiza mpaka ntchitoyo inatha+ ndiponso kufikira pamene ansembewo anadziyeretsa,+ popeza Alevi ankafunitsitsa kudziyeretsa kuposa ansembe.+

  • 2 Mbiri 30:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Hezekiya mfumu ya Yuda anapereka+ ku mpingowo ng’ombe zamphongo 1,000 ndi nkhosa 7,000. Akalonganso+ anapereka ku mpingowo ng’ombe zamphongo 1,000 ndi nkhosa 10,000, ndipo ansembe+ ambiri anali kudziyeretsa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena