2 Mbiri 30:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma panali anthu ambiri mumpingowo amene sanadziyeretse. Choncho Alevi+ ndi amene anali kugwira ntchito yophera nyama za pasika+ anthu onse amene sanali oyera, kuti awayeretse kwa Yehova.
17 Koma panali anthu ambiri mumpingowo amene sanadziyeretse. Choncho Alevi+ ndi amene anali kugwira ntchito yophera nyama za pasika+ anthu onse amene sanali oyera, kuti awayeretse kwa Yehova.