2 Mbiri 30:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo sanathe kuchita pasikayo m’mwezi woyamba+ popeza ansembe amene anadziyeretsa sanali okwanira+ komanso anthuwo sanasonkhane ku Yerusalemu.
3 Iwo sanathe kuchita pasikayo m’mwezi woyamba+ popeza ansembe amene anadziyeretsa sanali okwanira+ komanso anthuwo sanasonkhane ku Yerusalemu.