2 Mbiri 30:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo sanathe kuchita Pasikayo pa nthawi imene ankayenera kuchita+ chifukwa ansembe amene anadziyeretsa+ anali osakwanira komanso anthu anali asanasonkhane ku Yerusalemu.
3 Iwo sanathe kuchita Pasikayo pa nthawi imene ankayenera kuchita+ chifukwa ansembe amene anadziyeretsa+ anali osakwanira komanso anthu anali asanasonkhane ku Yerusalemu.