Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 8:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pambuyo pake, Aleviwo azitumikira pachihema chokumanako.+ Chotero uwayeretse, ndi kuwauza kuti ayende uku ndi uku monga nsembe yoweyula.+

  • Numeri 8:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ndipo ndidzapereka Alevi kwa Aroni ndi ana ake monga operekedwa kuchokera mwa ana a Isiraeli.+ Aleviwo adzatumikira m’malo mwa ana a Isiraeli pachihema chokumanako,+ ndipo aziphimba machimo a ana a Isiraeli.+ Chifukwa cha utumiki wawowo, mliri sudzawagwera ana a Isiraeli pakuti sadzayandikira malo oyerawo.”

  • Numeri 18:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Utengenso abale ako a fuko la Levi, amtundu wa bambo ako, kuti azikhala pafupi ndi inu. Azitumikira+ iweyo limodzi ndi ana ako pachihema cha Umboni.+

  • Numeri 18:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Inetu ndatenga abale anu Alevi, mwa ana a Isiraeli,+ ndipo ndawapereka kwa inu monga mphatso yanu.+ Iwowa akhala operekedwa kwa Yehova kuti atumikire pachihema chokumanako.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena