Numeri 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aleviwo uwapereke kwa Aroni ndi kwa ana ake. Amenewa ndi amene aperekedwa. Aperekedwa kwa iye kuchokera mwa ana a Isiraeli.+ Numeri 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inetu ndatenga abale anu Alevi, mwa ana a Isiraeli,+ ndipo ndawapereka kwa inu monga mphatso yanu.+ Iwowa akhala operekedwa kwa Yehova kuti atumikire pachihema chokumanako.+
9 Aleviwo uwapereke kwa Aroni ndi kwa ana ake. Amenewa ndi amene aperekedwa. Aperekedwa kwa iye kuchokera mwa ana a Isiraeli.+
6 Inetu ndatenga abale anu Alevi, mwa ana a Isiraeli,+ ndipo ndawapereka kwa inu monga mphatso yanu.+ Iwowa akhala operekedwa kwa Yehova kuti atumikire pachihema chokumanako.+