Aroma 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wochenjeza, aike mtima wake pa kuchenjeza.+ Wogawa, agawe mowolowa manja.+ Wotsogolera,+ atsogolere mwakhama. Ndipo wosonyeza chifundo,+ achite zimenezo mokondwa. 1 Akorinto 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Malinga ndi kukoma mtima kwakukulu+ kumene Mulungu anandisonyeza, ndinayala maziko+ monga woyang’anira wanzeru wa ntchito zomangamanga, koma amene akumanga pamaziko amenewo ndi munthu wina. Aliyense asamale mmene akumangirapo.+ Aheberi 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Muzimvera amene akutsogolera pakati panu+ ndipo muziwagonjera.+ Iwo amayang’anira miyoyo yanu monga anthu amene adzayankhe mlandu.+ Muziwamvera ndi kuwagonjera kuti agwire ntchito yawo mwachimwemwe, osati modandaula, pakuti akatero zingakhale zokuvulazani.+
8 Wochenjeza, aike mtima wake pa kuchenjeza.+ Wogawa, agawe mowolowa manja.+ Wotsogolera,+ atsogolere mwakhama. Ndipo wosonyeza chifundo,+ achite zimenezo mokondwa.
10 Malinga ndi kukoma mtima kwakukulu+ kumene Mulungu anandisonyeza, ndinayala maziko+ monga woyang’anira wanzeru wa ntchito zomangamanga, koma amene akumanga pamaziko amenewo ndi munthu wina. Aliyense asamale mmene akumangirapo.+
17 Muzimvera amene akutsogolera pakati panu+ ndipo muziwagonjera.+ Iwo amayang’anira miyoyo yanu monga anthu amene adzayankhe mlandu.+ Muziwamvera ndi kuwagonjera kuti agwire ntchito yawo mwachimwemwe, osati modandaula, pakuti akatero zingakhale zokuvulazani.+