Aroma 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndithudi, pochita zimenezi ndinatsimikiza mtima kuti ndisalengeze uthenga wabwino kumene Khristu anatchulidwa kale, ndi cholinga chakuti ndisamange pamaziko+ a munthu wina, Aheberi 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa chifukwa chimenechi, pamene tasiya chiphunzitso choyambirira+ cha Khristu+ tsopano, tiyeni tiyesetse mwakhama kuti tikhale okhwima mwauzimu.+ Tisayambe kuyalanso maziko,+ amene ndi kulapa ntchito zakufa,+ chikhulupiriro mwa Mulungu,+
20 Ndithudi, pochita zimenezi ndinatsimikiza mtima kuti ndisalengeze uthenga wabwino kumene Khristu anatchulidwa kale, ndi cholinga chakuti ndisamange pamaziko+ a munthu wina,
6 Pa chifukwa chimenechi, pamene tasiya chiphunzitso choyambirira+ cha Khristu+ tsopano, tiyeni tiyesetse mwakhama kuti tikhale okhwima mwauzimu.+ Tisayambe kuyalanso maziko,+ amene ndi kulapa ntchito zakufa,+ chikhulupiriro mwa Mulungu,+