15 Sitikudzitamandira kunja kwa malire a gawo limene tinapatsidwa, podzitamandira chifukwa cha ntchito za munthu wina ayi,+ koma tili ndi chiyembekezo chakuti chikhulupiriro chanu chikadzawonjezeka,+ ntchito yathunso idzakula pakati panu, limene ndi gawo lathu.+ Ndiyeno tidzachitanso zowonjezereka,