Aroma 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndithudi, pochita zimenezi ndinatsimikiza mtima kuti ndisalengeze uthenga wabwino kumene Khristu anatchulidwa kale, ndi cholinga chakuti ndisamange pamaziko+ a munthu wina,
20 Ndithudi, pochita zimenezi ndinatsimikiza mtima kuti ndisalengeze uthenga wabwino kumene Khristu anatchulidwa kale, ndi cholinga chakuti ndisamange pamaziko+ a munthu wina,