1 Akorinto 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Malinga ndi kukoma mtima kwakukulu+ kumene Mulungu anandisonyeza, ndinayala maziko+ monga woyang’anira wanzeru wa ntchito zomangamanga, koma amene akumanga pamaziko amenewo ndi munthu wina. Aliyense asamale mmene akumangirapo.+
10 Malinga ndi kukoma mtima kwakukulu+ kumene Mulungu anandisonyeza, ndinayala maziko+ monga woyang’anira wanzeru wa ntchito zomangamanga, koma amene akumanga pamaziko amenewo ndi munthu wina. Aliyense asamale mmene akumangirapo.+