Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Akorinto 13:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pamene ndinali kamwana, ndinali kulankhula ngati kamwana, kuganiza ngati kamwana, ndiponso kuona zinthu ngati kamwana. Koma tsopano pamene ndakula,+ ndasiya zachibwana.

  • 1 Akorinto 14:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Abale, musakhale ana aang’ono pa luntha la kuzindikira,+ koma khalani tiana pa zoipa,+ ndipo pa luntha la kuzindikira khalani aakulu msinkhu.+

  • Aefeso 4:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 kufikira tonse tidzafike pa umodzi m’chikhulupiriro komanso pa kumudziwa molondola Mwana wa Mulungu, inde, kufikira tidzakhale munthu wachikulire,+ wofika pa msinkhu wauchikulire umene Khristu anafikapo.+

  • Afilipi 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Komabe, mulimonse mmene tapitira patsogolo, tiyeni tipitirize kupita patsogolo mwa kuyenda moyenera+ m’njira yomweyo.

  • Aheberi 5:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma chakudya chotafuna ndi cha anthu okhwima mwauzimu, amene pogwiritsa ntchito mphamvu zawo za kuzindikira,+ aphunzitsa mphamvuzo kusiyanitsa choyenera ndi chosayenera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena