Aefeso 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 kufikira tonse tidzafike pa umodzi m’chikhulupiriro komanso pa kumudziwa molondola Mwana wa Mulungu, inde, kufikira tidzakhale munthu wachikulire,+ wofika pa msinkhu wauchikulire umene Khristu anafikapo.+ Aheberi 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa chifukwa chimenechi, pamene tasiya chiphunzitso choyambirira+ cha Khristu+ tsopano, tiyeni tiyesetse mwakhama kuti tikhale okhwima mwauzimu.+ Tisayambe kuyalanso maziko,+ amene ndi kulapa ntchito zakufa,+ chikhulupiriro mwa Mulungu,+
13 kufikira tonse tidzafike pa umodzi m’chikhulupiriro komanso pa kumudziwa molondola Mwana wa Mulungu, inde, kufikira tidzakhale munthu wachikulire,+ wofika pa msinkhu wauchikulire umene Khristu anafikapo.+
6 Pa chifukwa chimenechi, pamene tasiya chiphunzitso choyambirira+ cha Khristu+ tsopano, tiyeni tiyesetse mwakhama kuti tikhale okhwima mwauzimu.+ Tisayambe kuyalanso maziko,+ amene ndi kulapa ntchito zakufa,+ chikhulupiriro mwa Mulungu,+