1 Akorinto 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Inunso pitirizani kudzipereka kwa anthu ngati amenewo, ndi kwa aliyense wogwirizana nafe pa ntchitoyi, ndiponso wogwira ntchito molimbika.+ Aefeso 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Gonjeranani+ poopa Khristu. 1 Petulo 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chimodzimodzinso inu anyamata. Muzigonjera+ amuna achikulire. Koma nonsenu muzichitirana zinthu modzichepetsa,+ chifukwa Mulungu amatsutsa odzikweza, koma odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.+
16 Inunso pitirizani kudzipereka kwa anthu ngati amenewo, ndi kwa aliyense wogwirizana nafe pa ntchitoyi, ndiponso wogwira ntchito molimbika.+
5 Chimodzimodzinso inu anyamata. Muzigonjera+ amuna achikulire. Koma nonsenu muzichitirana zinthu modzichepetsa,+ chifukwa Mulungu amatsutsa odzikweza, koma odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.+