31 Iwonso anachita maere+ mofanana ndi mmene abale awo, ana a Aroni, anachitira pamaso pa Davide mfumu, Zadoki, Ahimeleki, ndiponso pamaso pa atsogoleri a nyumba za makolo za ansembe ndi za Alevi. Nyumba ya makolo+ ya wamkulu inali chimodzimodzi ndi nyumba ya makolo ya wamng’ono.