1 Mbiri 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Panalinso alonda 4,000 a pachipata+ ndi anthu 4,000 oimbira Yehova zitamando+ ndi zoimbira+ zimene Davide anati, “Zimenezi ndazipanga kuti tizitamandira Mulungu.”
5 Panalinso alonda 4,000 a pachipata+ ndi anthu 4,000 oimbira Yehova zitamando+ ndi zoimbira+ zimene Davide anati, “Zimenezi ndazipanga kuti tizitamandira Mulungu.”