1 Mbiri 6:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Nawa anthu amene Davide+ anawapatsa udindo wotsogolera kuimba panyumba ya Yehova ataikapo Likasa.+ 1 Mbiri 9:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Amenewa ndiwo anali oimba,+ atsogoleri a makolo a Alevi m’zipinda zodyera.+ Iwo sanali kupatsidwa ntchito zina+ chifukwa usana ndi usiku anali ndi udindo wogwira ntchito yawo.+
31 Nawa anthu amene Davide+ anawapatsa udindo wotsogolera kuimba panyumba ya Yehova ataikapo Likasa.+
33 Amenewa ndiwo anali oimba,+ atsogoleri a makolo a Alevi m’zipinda zodyera.+ Iwo sanali kupatsidwa ntchito zina+ chifukwa usana ndi usiku anali ndi udindo wogwira ntchito yawo.+