2 Samueli 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno analowetsa likasa la Yehova muhema limene Davide anamanga n’kuika likasalo pamalo ake muhemalo.+ Kenako Davide anapereka kwa Yehova nsembe zopsereza+ ndi nsembe zachiyanjano.+ Salimo 132:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Awa ndi malo anga okhalamo mpaka muyaya.+Ndidzakhala mmenemu, pakuti ndimafunitsitsa kukhala m’malo amenewa.+
17 Ndiyeno analowetsa likasa la Yehova muhema limene Davide anamanga n’kuika likasalo pamalo ake muhemalo.+ Kenako Davide anapereka kwa Yehova nsembe zopsereza+ ndi nsembe zachiyanjano.+
14 “Awa ndi malo anga okhalamo mpaka muyaya.+Ndidzakhala mmenemu, pakuti ndimafunitsitsa kukhala m’malo amenewa.+