Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 46:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Mulungu ali pakati pa mzinda.+ Mzindawo sudzagwedezeka.+

      Mulungu adzauthandiza m’bandakucha.+

  • Salimo 68:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 N’chifukwa chiyani inu mapiri a nsonga zitalizitali mumayang’ana mwanjiru

      Phiri limene Mulungu wafuna kukhalamo?+

      Yehova adzakhala m’phiri limenelo mpaka muyaya.+

  • Yesaya 24:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Mwezi wathunthu wachita manyazi. Dzuwa lowala lachitanso manyazi,+ pakuti Yehova wa makamu wakhala mfumu+ yaulemerero m’phiri la Ziyoni+ ndi mu Yerusalemu, pamaso pa anthu ake achikulire.+

  • Yoweli 3:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Magazi awo amene anali ndi mlandu adzakhala opanda mlandu,+ ndipo Yehova azidzakhala mu Ziyoni.”+

  • Zekariya 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Fuula kwambiri ndi kusangalala, iwe mwana wamkazi wa Ziyoni,+ pakuti ine ndikubwera+ ndipo ndidzakhala mwa iwe,”+ watero Yehova.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena