1 Mbiri 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu okhala ku Yebusiwo anayamba kuuza Davide kuti: “Sulowa mumzinda uno.”+ Ngakhale zinali choncho, Davide analanda Ziyoni,+ malo okhala mumpanda wolimba kwambiri, umene ndi Mzinda wa Davide.+ Salimo 48:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Phiri la Ziyoni limene lili m’dera lakutali la kumpoto,+Ndi lokongola chifukwa lili pamalo okwezeka ndi osangalatsa padziko lonse lapansi,+Mudzi wa Mfumu Yaikulu.+ Salimo 132:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova wasankha Ziyoni,+Ndipo amafunitsitsa kuti akhale malo ake okhalamo. Iye amati:+
5 Anthu okhala ku Yebusiwo anayamba kuuza Davide kuti: “Sulowa mumzinda uno.”+ Ngakhale zinali choncho, Davide analanda Ziyoni,+ malo okhala mumpanda wolimba kwambiri, umene ndi Mzinda wa Davide.+
2 Phiri la Ziyoni limene lili m’dera lakutali la kumpoto,+Ndi lokongola chifukwa lili pamalo okwezeka ndi osangalatsa padziko lonse lapansi,+Mudzi wa Mfumu Yaikulu.+