Salimo 97:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 97 Yehova wakhala mfumu!+ Dziko lapansi likondwere,+Ndipo zilumba zambiri zisangalale.+ Chivumbulutso 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ndi mawu akuti: “Tikukuyamikani+ inu Yehova, Mulungu Wamphamvuyonse,+ Inu amene mulipo+ ndi amene munalipo, chifukwa mwatenga mphamvu yanu yaikulu+ ndi kuyamba kulamulira monga mfumu.+
17 ndi mawu akuti: “Tikukuyamikani+ inu Yehova, Mulungu Wamphamvuyonse,+ Inu amene mulipo+ ndi amene munalipo, chifukwa mwatenga mphamvu yanu yaikulu+ ndi kuyamba kulamulira monga mfumu.+