Salimo 103:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Sanatichitire mogwirizana ndi machimo athu,+Kapena kutipatsa chilango chogwirizana ndi zolakwa zathu.+ Yesaya 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova, pogwiritsa ntchito mzimu wa chiweruzo ndi mzimu wa moto,+ adzatsuka nyansi za ana aakazi a Ziyoni,+ ndiponso adzatsuka+ mkati mwa Yerusalemu n’kuchotsamo magazi amene Yerusalemuyo anakhetsa.+ Ezekieli 36:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ine ndidzakuwazani madzi oyera ndipo mudzakhala oyera. Ndidzakuyeretsani+ pokuchotserani zonyansa zanu zonse+ ndi mafano anu onse onyansa.+ Mika 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Inu mudzatichitiranso chifundo+ ndipo mudzapondaponda zolakwa zathu.+ Machimo athu onse mudzawaponya pakati pa nyanja yozama.+
10 Sanatichitire mogwirizana ndi machimo athu,+Kapena kutipatsa chilango chogwirizana ndi zolakwa zathu.+
4 Yehova, pogwiritsa ntchito mzimu wa chiweruzo ndi mzimu wa moto,+ adzatsuka nyansi za ana aakazi a Ziyoni,+ ndiponso adzatsuka+ mkati mwa Yerusalemu n’kuchotsamo magazi amene Yerusalemuyo anakhetsa.+
25 Ine ndidzakuwazani madzi oyera ndipo mudzakhala oyera. Ndidzakuyeretsani+ pokuchotserani zonyansa zanu zonse+ ndi mafano anu onse onyansa.+
19 Inu mudzatichitiranso chifundo+ ndipo mudzapondaponda zolakwa zathu.+ Machimo athu onse mudzawaponya pakati pa nyanja yozama.+