Ezara 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano pambuyo pa zonse zimene zatigwera chifukwa cha zochita zathu zoipa+ ndi machimo athu ochuluka, ngakhale kuti inuyo Mulungu wathu simunatilange monga mmene tinafunika kulangidwira+ ndipo mwalola kuti anthu onsewa apulumuke,+ Salimo 130:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Ya, mukanakhala kuti mumayang’anitsitsa zolakwa,+Ndani akanaima pamaso panu, inu Yehova?+ Yesaya 55:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munthu woipa asiye njira yake+ ndipo wopweteka anzake asiye maganizo ake.+ Iye abwerere kwa Yehova ndipo adzamuchitira chifundo.+ Abwerere kwa Mulungu wathu, pakuti amakhululuka ndi mtima wonse.+
13 Tsopano pambuyo pa zonse zimene zatigwera chifukwa cha zochita zathu zoipa+ ndi machimo athu ochuluka, ngakhale kuti inuyo Mulungu wathu simunatilange monga mmene tinafunika kulangidwira+ ndipo mwalola kuti anthu onsewa apulumuke,+
7 Munthu woipa asiye njira yake+ ndipo wopweteka anzake asiye maganizo ake.+ Iye abwerere kwa Yehova ndipo adzamuchitira chifundo.+ Abwerere kwa Mulungu wathu, pakuti amakhululuka ndi mtima wonse.+