Salimo 103:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Sanatichitire mogwirizana ndi machimo athu,+Kapena kutipatsa chilango chogwirizana ndi zolakwa zathu.+ Maliro 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa cha kukoma mtima kosatha+ kwa Yehova, ife sitinafafanizidwe,+ ndipo chifundo chake sichidzatha.+ Maliro 3:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Kodi munthu angadandaulirenji+ chifukwa cha zotsatirapo za tchimo lake?+
10 Sanatichitire mogwirizana ndi machimo athu,+Kapena kutipatsa chilango chogwirizana ndi zolakwa zathu.+
22 Chifukwa cha kukoma mtima kosatha+ kwa Yehova, ife sitinafafanizidwe,+ ndipo chifundo chake sichidzatha.+