Salimo 46:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mulungu ali mumzindawo+ ndipo sungagonjetsedwe. Mulungu adzauthandiza mʼbandakucha.+