Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 8:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Chifukwa cha mtambowo, ansembewo+ analephera kupitiriza kutumikira,+ popeza ulemerero+ wa Yehova unadzaza nyumba ya Yehovayo.+

  • Salimo 46:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Mulungu ali pakati pa mzinda.+ Mzindawo sudzagwedezeka.+

      Mulungu adzauthandiza m’bandakucha.+

  • Yesaya 12:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Fuula mwachisangalalo iwe mkazi wokhala mu Ziyoni, pakuti Woyera wa Isiraeli ndi wamkulu pakati pako.”+

  • Mika 4:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Anthu amene anali kuyenda motsimphina ndidzawasonkhanitsanso pamodzi monga anthu otsala.+ Anthu amene anawachotsa m’dziko lawo ndi kuwapititsa kutali ndidzawasandutsa mtundu wamphamvu.+ Yehova adzawalamulira monga mfumu m’phiri la Ziyoni kuyambira nthawi imeneyo mpaka kalekale.+

  • Zekariya 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Fuula kwambiri ndi kusangalala, iwe mwana wamkazi wa Ziyoni,+ pakuti ine ndikubwera+ ndipo ndidzakhala mwa iwe,”+ watero Yehova.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena