Ekisodo 40:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Mose sanathenso kulowa m’chihema chokumanako, chifukwa mtambo+ unaphimba chihemacho ndipo munadzaza ulemerero wa Yehova.+ 2 Mbiri 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chifukwa cha mtambowo,+ ansembewo analephera kupitiriza kutumikira, popeza ulemerero+ wa Yehova unadzaza nyumba ya Mulungu woona. Ezekieli 44:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako ananditengera kutsogolo kwa Nyumba ija kudzera pachipata cha kumpoto kuti ndikaone zimene zinali kumeneko. Kumeneko ndinaona ulemerero wa Yehova utadzaza m’nyumba ya Yehova.+ Pamenepo ndinagwada n’kuwerama mpaka nkhope yanga pansi.+
35 Mose sanathenso kulowa m’chihema chokumanako, chifukwa mtambo+ unaphimba chihemacho ndipo munadzaza ulemerero wa Yehova.+
14 Chifukwa cha mtambowo,+ ansembewo analephera kupitiriza kutumikira, popeza ulemerero+ wa Yehova unadzaza nyumba ya Mulungu woona.
4 Kenako ananditengera kutsogolo kwa Nyumba ija kudzera pachipata cha kumpoto kuti ndikaone zimene zinali kumeneko. Kumeneko ndinaona ulemerero wa Yehova utadzaza m’nyumba ya Yehova.+ Pamenepo ndinagwada n’kuwerama mpaka nkhope yanga pansi.+