Ekisodo 40:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Mose sanathenso kulowa m’chihema chokumanako, chifukwa mtambo+ unaphimba chihemacho ndipo munadzaza ulemerero wa Yehova.+ 2 Mbiri 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chotero ansembe sanathe kulowa m’nyumba ya Yehova+ chifukwa ulemerero wa Yehova unadzaza nyumba ya Yehova.
35 Mose sanathenso kulowa m’chihema chokumanako, chifukwa mtambo+ unaphimba chihemacho ndipo munadzaza ulemerero wa Yehova.+
2 Chotero ansembe sanathe kulowa m’nyumba ya Yehova+ chifukwa ulemerero wa Yehova unadzaza nyumba ya Yehova.