Yoswa 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ndipo Yoswa anawachitira maere pamaso pa Yehova+ ku Silo. Kumeneko Yoswa anagawa dzikolo n’kupereka gawo limodzilimodzi ku mafuko a ana a Isiraeli.+ 1 Mbiri 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako anachita maere+ powagawira ntchito yoti azichita. Pochita maerewo, onse anali chimodzimodzi. Sanali kuyang’ana kuti uyu ndi wamng’ono kapena wamkulu,+ katswiri+ kapena wophunzira kumene. Miyambo 16:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Maere amaponyedwa pamwendo,+ koma zonse zimene maerewo amasonyeza zimachokera kwa Yehova.+ Machitidwe 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Atatero anachita maere+ pa iwo, ndipo maerewo anagwera Matiya. Choncho iye anamuphatikiza pa atumwi 11+ aja.
10 ndipo Yoswa anawachitira maere pamaso pa Yehova+ ku Silo. Kumeneko Yoswa anagawa dzikolo n’kupereka gawo limodzilimodzi ku mafuko a ana a Isiraeli.+
8 Kenako anachita maere+ powagawira ntchito yoti azichita. Pochita maerewo, onse anali chimodzimodzi. Sanali kuyang’ana kuti uyu ndi wamng’ono kapena wamkulu,+ katswiri+ kapena wophunzira kumene.
26 Atatero anachita maere+ pa iwo, ndipo maerewo anagwera Matiya. Choncho iye anamuphatikiza pa atumwi 11+ aja.