Ezekieli 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pita pakati pa anthu otengedwa ukapolo,+ pakati pa ana a anthu a mtundu wako, ndipo ukawauze kuti, ‘Izi n’zimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena,’ kaya akamve kapena ayi.”+
11 Pita pakati pa anthu otengedwa ukapolo,+ pakati pa ana a anthu a mtundu wako, ndipo ukawauze kuti, ‘Izi n’zimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena,’ kaya akamve kapena ayi.”+