Ezekieli 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kaya iwowo akamvetsera+ kapena ayi,+ pakuti iwo ndi nyumba yopanduka,+ adzadziwabe kuti pakati pawo panali mneneri.+ Machitidwe 20:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Choncho mukhale mboni lero, kuti ine ndine woyera pa mlandu wa magazi+ a anthu onse.
5 Kaya iwowo akamvetsera+ kapena ayi,+ pakuti iwo ndi nyumba yopanduka,+ adzadziwabe kuti pakati pawo panali mneneri.+