Ezekieli 33:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma mawu ako akadzakwaniritsidwa, pakuti adzakwaniritsidwa ndithu,+ iwo adzadziwa kuti pakati pawo panalidi mneneri.”+ Yohane 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndikanapanda kubwera kudzalankhula nawo, akanakhala opanda tchimo,+ koma tsopano alibe chodzilungamitsira pa tchimo lawo.+
33 Koma mawu ako akadzakwaniritsidwa, pakuti adzakwaniritsidwa ndithu,+ iwo adzadziwa kuti pakati pawo panalidi mneneri.”+
22 Ndikanapanda kubwera kudzalankhula nawo, akanakhala opanda tchimo,+ koma tsopano alibe chodzilungamitsira pa tchimo lawo.+