2 Mafumu 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Elisa munthu wa Mulungu woona atangomva kuti mfumu ya Isiraeli yang’amba zovala zake,+ anatumiza uthenga kwa mfumuyo, wakuti: “N’chifukwa chiyani mwang’amba zovala zanu? Muuzeni abwere kwa ine kuti adziwe kuti ku Isiraeli kuli mneneri.”+ Ezekieli 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kaya iwowo akamvetsera+ kapena ayi,+ pakuti iwo ndi nyumba yopanduka,+ adzadziwabe kuti pakati pawo panali mneneri.+
8 Elisa munthu wa Mulungu woona atangomva kuti mfumu ya Isiraeli yang’amba zovala zake,+ anatumiza uthenga kwa mfumuyo, wakuti: “N’chifukwa chiyani mwang’amba zovala zanu? Muuzeni abwere kwa ine kuti adziwe kuti ku Isiraeli kuli mneneri.”+
5 Kaya iwowo akamvetsera+ kapena ayi,+ pakuti iwo ndi nyumba yopanduka,+ adzadziwabe kuti pakati pawo panali mneneri.+