Ezekieli 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pita pakati pa anthu otengedwa ukapolo,+ pakati pa ana a anthu a mtundu wako, ndipo ukawauze kuti, ‘Izi n’zimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena,’ kaya akamve kapena ayi.”+ Ezekieli 33:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 munthu akamva kulira kwa lipengalo koma osachitapo kanthu,+ lupanga n’kubwera ndi kumupha, magazi ake adzakhala pamutu pake.+
11 Pita pakati pa anthu otengedwa ukapolo,+ pakati pa ana a anthu a mtundu wako, ndipo ukawauze kuti, ‘Izi n’zimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena,’ kaya akamve kapena ayi.”+
4 munthu akamva kulira kwa lipengalo koma osachitapo kanthu,+ lupanga n’kubwera ndi kumupha, magazi ake adzakhala pamutu pake.+