Ezekieli 33:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndikauza munthu woipa kuti, ‘Munthu woipa iwe, udzafa ndithu,’+ koma iwe osanena mawu alionse ochenjeza woipayo kuti asiye njira yake,+ iyeyo poti ndi woipa adzafa chifukwa cha zolakwa zake,+ koma magazi ake ndidzawafuna kuchokera m’manja mwako. Machitidwe 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma iwo atapitiriza kumutsutsa ndi kulankhula monyoza,+ iye anakutumula zovala zake+ ndi kuwauza kuti: “Magazi anu+ akhale pamitu panu. Ine ndilibe mlandu.+ Kuyambira tsopano ndizipita kwa anthu a mitundu ina.”+ 2 Akorinto 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tipatseni malo m’mitima mwanu.+ Ifetu sitinalakwire aliyense, sitinaipitse aliyense, ndipo sitinachenjerere aliyense.+
8 Ndikauza munthu woipa kuti, ‘Munthu woipa iwe, udzafa ndithu,’+ koma iwe osanena mawu alionse ochenjeza woipayo kuti asiye njira yake,+ iyeyo poti ndi woipa adzafa chifukwa cha zolakwa zake,+ koma magazi ake ndidzawafuna kuchokera m’manja mwako.
6 Koma iwo atapitiriza kumutsutsa ndi kulankhula monyoza,+ iye anakutumula zovala zake+ ndi kuwauza kuti: “Magazi anu+ akhale pamitu panu. Ine ndilibe mlandu.+ Kuyambira tsopano ndizipita kwa anthu a mitundu ina.”+
2 Tipatseni malo m’mitima mwanu.+ Ifetu sitinalakwire aliyense, sitinaipitse aliyense, ndipo sitinachenjerere aliyense.+