Numeri 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Bambo athu anafera m’chipululu.+ Koma iwo sanali nawo m’gulu la Kora+ limene linasonkhana kuti litsutsane ndi Yehova. Bambo athuwo anafa chifukwa cha tchimo lawo,+ ndipo pa nthawiyo analibe mwana aliyense wamwamuna. Miyambo 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ngakhale dzanja ligwirane ndi dzanja linzake, munthu woipa sadzapewa chilango,+ koma ana a anthu olungama adzapulumuka ndithu.+ Mlaliki 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma woipayo sizidzamuyendera bwino n’komwe,+ ndiponso sadzachulukitsa masiku ake amene ali ngati mthunzi,+ chifukwa saopa Mulungu.+
3 “Bambo athu anafera m’chipululu.+ Koma iwo sanali nawo m’gulu la Kora+ limene linasonkhana kuti litsutsane ndi Yehova. Bambo athuwo anafa chifukwa cha tchimo lawo,+ ndipo pa nthawiyo analibe mwana aliyense wamwamuna.
21 Ngakhale dzanja ligwirane ndi dzanja linzake, munthu woipa sadzapewa chilango,+ koma ana a anthu olungama adzapulumuka ndithu.+
13 Koma woipayo sizidzamuyendera bwino n’komwe,+ ndiponso sadzachulukitsa masiku ake amene ali ngati mthunzi,+ chifukwa saopa Mulungu.+