Numeri 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Bambo athu anafera mʼchipululu. Koma iwo sanali mʼgulu la anthu amene ankatsatira Kora,+ omwe anasonkhana kuti atsutsane ndi Yehova. Bambo athuwo anafa chifukwa cha tchimo lawo, ndipo analibe mwana aliyense wamwamuna.
3 “Bambo athu anafera mʼchipululu. Koma iwo sanali mʼgulu la anthu amene ankatsatira Kora,+ omwe anasonkhana kuti atsutsane ndi Yehova. Bambo athuwo anafa chifukwa cha tchimo lawo, ndipo analibe mwana aliyense wamwamuna.