Ezekieli 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamverani! Miyoyo yonse ndi yanga.+ Moyo+ wa bambo komanso moyo wa mwana, yonse ndi yanga.+ Moyo umene ukuchimwawo+ ndi umene udzafe.+ Aroma 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiye chifukwa chake monga mmene uchimo unalowera m’dziko kudzera mwa munthu mmodzi,+ ndi imfa+ kudzera mwa uchimo, imfayo n’kufalikira kwa anthu onse chifukwa onse anachimwa+ . . . Aroma 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chifukwa malipiro a uchimo ndi imfa,+ koma mphatso+ imene Mulungu amapereka ndi moyo wosatha+ kudzera mwa Khristu Yesu Ambuye wathu.+
4 Tamverani! Miyoyo yonse ndi yanga.+ Moyo+ wa bambo komanso moyo wa mwana, yonse ndi yanga.+ Moyo umene ukuchimwawo+ ndi umene udzafe.+
12 Ndiye chifukwa chake monga mmene uchimo unalowera m’dziko kudzera mwa munthu mmodzi,+ ndi imfa+ kudzera mwa uchimo, imfayo n’kufalikira kwa anthu onse chifukwa onse anachimwa+ . . .
23 Chifukwa malipiro a uchimo ndi imfa,+ koma mphatso+ imene Mulungu amapereka ndi moyo wosatha+ kudzera mwa Khristu Yesu Ambuye wathu.+