Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndidzabweretsa lupanga pa inu lobwezera chilango+ chifukwa cha pangano.+ Pamenepo mudzathawira m’mizinda yanu, ndipo ndidzakutumizirani mliri pakati panu+ ndi kukuperekani m’manja mwa mdani.+

  • Yeremiya 25:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 “‘Phokoso lidzamveka kumalekezero a dziko lapansi, pakuti Yehova akufuna kuimba mlandu mitundu ya anthu.+ Iye mwini adzalimbana ndi anthu onse powaweruza.+ Anthu oipa adzawapha ndi lupanga,’+ watero Yehova.

  • Ezekieli 6:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Unene kuti, ‘Inu mapiri a Isiraeli, imvani mawu a Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa:+ Izi n’zimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kwa mapiri, zitunda,+ mitsinje ndi zigwa: “Ine ndidzakubweretserani lupanga ndipo ndidzawononga malo anu okwezeka.+

  • Ezekieli 14:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “‘Kapena nditati ndibweretse lupanga m’dzikolo,+ n’kunena kuti: “M’dzikolo mudutse lupanga,” ine n’kuphamo anthu ndi ziweto,+

  • Ezekieli 21:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Iwe mwana wa munthu, losera kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Nena mofuula kuti, ‘Lupanga! Lupanga!+ Lupanga lanoledwa+ ndi kupukutidwa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena