Ezekieli 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘Kapena nditati ndibweretse lupanga mʼdzikolo,+ nʼkunena kuti: “Mʼdzikolo mudutse lupanga,” ine nʼkuphamo anthu ndi ziweto,+
17 “‘Kapena nditati ndibweretse lupanga mʼdzikolo,+ nʼkunena kuti: “Mʼdzikolo mudutse lupanga,” ine nʼkuphamo anthu ndi ziweto,+