Yeremiya 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndithudi, zitunda ndi chipwirikiti chimene chimachitika m’mapiri+ ndiko kupembedza kwachinyengo.+ Kunena zoona chipulumutso cha Isiraeli chili mwa Yehova Mulungu wathu.+ Yeremiya 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 ndi pamapiri. Katundu wanu ndi chuma chanu chonse ndidzazipereka kuti anthu azifunkhe.+ Ndidzapereka malo anu okwezeka chifukwa cha tchimo limene lachitika m’madera anu onse.+
23 Ndithudi, zitunda ndi chipwirikiti chimene chimachitika m’mapiri+ ndiko kupembedza kwachinyengo.+ Kunena zoona chipulumutso cha Isiraeli chili mwa Yehova Mulungu wathu.+
3 ndi pamapiri. Katundu wanu ndi chuma chanu chonse ndidzazipereka kuti anthu azifunkhe.+ Ndidzapereka malo anu okwezeka chifukwa cha tchimo limene lachitika m’madera anu onse.+