2 Mafumu 24:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mfumu ya Babulo inatenga chuma chonse cha m’nyumba ya Yehova ndi chuma cha m’nyumba ya mfumu.+ Inaphwanyaphwanyanso ziwiya zonse+ zagolide zimene Solomo mfumu ya Isiraeli anapangira kachisi wa Yehova, monga momwe Yehova ananenera. Yeremiya 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndidzapereka chuma chanu anthu inu ndi zinthu zanu zamtengo wapatali kwa wofunkha+ popanda malipiro. Ndidzatero chifukwa cha machimo anu onse amene munachita m’dziko lanu lonse.+
13 Mfumu ya Babulo inatenga chuma chonse cha m’nyumba ya Yehova ndi chuma cha m’nyumba ya mfumu.+ Inaphwanyaphwanyanso ziwiya zonse+ zagolide zimene Solomo mfumu ya Isiraeli anapangira kachisi wa Yehova, monga momwe Yehova ananenera.
13 Ndidzapereka chuma chanu anthu inu ndi zinthu zanu zamtengo wapatali kwa wofunkha+ popanda malipiro. Ndidzatero chifukwa cha machimo anu onse amene munachita m’dziko lanu lonse.+